Levitiko 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, moto unatsika kuchokera kwa Yehova ndi kuwawononga,+ moti anafa pamaso pa Yehova.+ 1 Mbiri 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Uza, ndipo anamupha chifukwa anatambasula dzanja lake n’kugwira Likasa,+ moti Uza anafera pomwepo pamaso pa Mulungu.+ Machitidwe 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hananiya atamva mawu amenewa anagwa pansi ndi kumwalira.+ Ndipo onse amene anamva zimenezi anagwidwa ndi mantha aakulu.+
10 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Uza, ndipo anamupha chifukwa anatambasula dzanja lake n’kugwira Likasa,+ moti Uza anafera pomwepo pamaso pa Mulungu.+
5 Hananiya atamva mawu amenewa anagwa pansi ndi kumwalira.+ Ndipo onse amene anamva zimenezi anagwidwa ndi mantha aakulu.+