Levitiko 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musamalumbire zabodza m’dzina langa+ ndi kuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova. Miyambo 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+ Ezekieli 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndidzamva chisoni chifukwa cha dzina langa loyera limene nyumba ya Isiraeli yalidetsa pakati pa anthu a mitundu ina kumene iwo anapita.”+
9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+
21 Ndidzamva chisoni chifukwa cha dzina langa loyera limene nyumba ya Isiraeli yalidetsa pakati pa anthu a mitundu ina kumene iwo anapita.”+