Ekisodo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo iye analandira golideyo kuchokera kwa anthuwo ndipo pogwiritsa ntchito chosemera, anam’panga+ kukhala fano la mwana wa ng’ombe+ lopangidwa ndi golide wosungunula. Zitatero iwo anayamba kunena kuti: “Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ Danieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
4 Pamenepo iye analandira golideyo kuchokera kwa anthuwo ndipo pogwiritsa ntchito chosemera, anam’panga+ kukhala fano la mwana wa ng’ombe+ lopangidwa ndi golide wosungunula. Zitatero iwo anayamba kunena kuti: “Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+