Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo oweruza azifufuza nkhaniyo mosamala.+ Mboniyo ikapezeka kuti ndi yonama ndipo yaneneza m’bale wake mlandu wonama,

  • Miyambo 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,+ ndipo wolankhula mabodza sadzapulumuka.+

  • Mateyu 26:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni wonama kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha+

  • Machitidwe 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako mwamseri ananyengerera amuna ena kuti anene kuti:+ “Tamumva ife ameneyu akulankhula mawu onyoza+ Mose ndi Mulungu.”

  • Chivumbulutso 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndipo ndinamva mawu ofuula kumwamba, akuti:

      “Tsopano chipulumutso,+ mphamvu,+ ufumu wa Mulungu wathu,+ ndi ulamuliro wa Khristu+ wake zafika, chifukwa woneneza abale athu waponyedwa pansi. Iyeyo anali kuwaneneza usana ndi usiku pamaso pa Mulungu wathu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena