Ekisodo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma, azambawo anali oopa Mulungu+ woona, ndipo sanachite zimene mfumu ya Iguputo inawauza.+ M’malomwake, ana aamuna anali kuwasiya amoyo.+ Levitiko 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamachitirane chinyengo,+ ndipo muziopa Mulungu wanu,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
17 Koma, azambawo anali oopa Mulungu+ woona, ndipo sanachite zimene mfumu ya Iguputo inawauza.+ M’malomwake, ana aamuna anali kuwasiya amoyo.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.