Ekisodo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lino limene munatuluka mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova anakutulutsani mmenemo ndi mphamvu ya dzanja lake.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+ Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Luka 1:74 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 kuti pambuyo pakuti tapulumutsidwa m’manja mwa adani,+ atipatse mwayi wochita utumiki wopatulika kwa iye+ mopanda mantha,
3 Chotero Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lino limene munatuluka mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova anakutulutsani mmenemo ndi mphamvu ya dzanja lake.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+
74 kuti pambuyo pakuti tapulumutsidwa m’manja mwa adani,+ atipatse mwayi wochita utumiki wopatulika kwa iye+ mopanda mantha,