Deuteronomo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+ Oweruza 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira.
33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+
3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira.