7 Simuyenera kudya mitundu iyi yokha mwa nyama zonse zimene zimabzikula kapena zokhala ndi ziboda zogawanika, zokhala ndi mpata pakati: ngamila,+ kalulu+ ndi mbira,+ chifukwa zimabzikula koma si zogawanika ziboda. Nyama zimenezi n’zodetsedwa kwa inu.