3 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake,+ popeza ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.
29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu, nsembe yamachimo ndi nsembe ya kupalamula.+ Chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+