-
Levitiko 13:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Ndiyeno pa tsiku la 7, wansembe azionanso munthuyo kachiwiri. Ngati nthendayo yayamba kuzimiririka ndipo sinafalikire pakhungu, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera. Inali chabe nkhanambo. Munthuyo azichapa zovala zake ndi kukhala woyera.
-