Levitiko 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako. Levitiko 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako.
16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako.
26 Wansembe amene waipereka monga nsembe yamachimo aziidya.+ Aziidyera kumalo oyera,+ m’bwalo+ la chihema chokumanako.