59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi, amene mkazi wake anam’berekera ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mlongo wawo Miriamu.+
4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+