Genesis 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo. Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu+ aja anamwalirira.+
6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo.