Numeri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+
22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+