Ekisodo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo ndidziwa bwanji kuti mwandikomera mtima, ineyo ndi anthu anu? Si mwa kuyenda nafe kodi?+ Pajatu ine ndi anthu anu mwatisiyanitsa ndi anthu ena onse amene ali padziko lapansi.”+ Deuteronomo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+
16 Ndipo ndidziwa bwanji kuti mwandikomera mtima, ineyo ndi anthu anu? Si mwa kuyenda nafe kodi?+ Pajatu ine ndi anthu anu mwatisiyanitsa ndi anthu ena onse amene ali padziko lapansi.”+
8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+