Numeri 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amenewa ndiwo anali olembedwa mayina a ana a Isiraeli, malinga ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse olembedwa mayina m’misasa yonse, analipo 603,550.+ Numeri 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane.+ Tsopano bwerani, mudzanditembererere anthuwa,+ kuti mwina ndingathe kumenyana nawo n’kuwathamangitsa.’”
32 Amenewa ndiwo anali olembedwa mayina a ana a Isiraeli, malinga ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse olembedwa mayina m’misasa yonse, analipo 603,550.+
11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane.+ Tsopano bwerani, mudzanditembererere anthuwa,+ kuti mwina ndingathe kumenyana nawo n’kuwathamangitsa.’”