Numeri 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amenewa ndi Aisiraeli amene mayina awo analembedwa, mogwirizana ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse amene analembedwa mayina mʼmagulu onse, analipo 603,550.+
32 Amenewa ndi Aisiraeli amene mayina awo analembedwa, mogwirizana ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse amene analembedwa mayina mʼmagulu onse, analipo 603,550.+