Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 27:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma Isaki anayankha Esau kuti: “Taona, iye uja ndamuika kukhala mbuye wako.+ Ndamupatsanso abale ake onse kuti akhale atumiki ake.+ Komanso ndam’dalitsira zokolola zake ndi vinyo wake watsopano.+ Nanga chatsalanso n’chiyani choti ndikuchitire mwana wanga?”

  • 2 Samueli 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu.+ Mu Edomu yense anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+

  • 1 Mbiri 18:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho anakhazikitsa midzi ya asilikali mu Edomu, ndipo Aedomu onse anakhala akapolo a Davide.+ Yehova anali kupulumutsa Davide kulikonse kumene anali kupita.+

  • Salimo 60:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+

      Ndidzaponyera Edomu nsapato zanga.+

      Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+

  • Yesaya 34:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Pakuti lupanga langa+ lidzakhala magazi okhaokha kumwambako. Lupangalo lidzatsikira pa Edomu+ ndi pa anthu amene ndikufuna kuwawononga+ mogwirizana ndi chilungamo changa.

  • Amosi 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga adzatenge zinthu zotsala za Edomu+ ndi mitundu yonse ya anthu imene inali kuitanira pa dzina langa,’+ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena