Numeri 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano. Numeri 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anatengera anthu ogwidwawo limodzi ndi zofunkha zina zonse kwa Mose, wansembe Eleazara, ndi kwa khamu la ana a Isiraeli. Anapita nawo kumsasa wawo ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+ Numeri 33:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu n’kukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+
22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.
12 Anatengera anthu ogwidwawo limodzi ndi zofunkha zina zonse kwa Mose, wansembe Eleazara, ndi kwa khamu la ana a Isiraeli. Anapita nawo kumsasa wawo ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+
48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu n’kukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+