Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “‘M’bale wanu akasauka n’kugulitsa ena mwa malo ake, wowombola amene ndi wachibale wake wapafupi azibwera ndi kugulanso zimene m’bale wakeyo anagulitsa.+

  • Levitiko 25:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Komanso m’bale wa bambo ake, mwana wa m’bale wa bambo akewo, wachibale wake aliyense wapafupi,+ kapena kuti aliyense wa m’banja lake angathe kumuwombola.

      “‘Kapenanso mwiniwakeyo akalemera, azidziwombola.+

  • Rute 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Boazi anauza wowombola+ uja kuti: “Naomi amene wabwerera kuchokera kudziko la Mowabu+ ayenera kugulitsa munda umene unali wa m’bale wathu Elimeleki.+

  • Yeremiya 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Hanameli mwana wa m’bale wa bambo anga analowa m’Bwalo la Alonda+ ndipo anandipeza mogwirizana ndi mawu a Yehova. Pamenepo iye anati: “Gula munda wanga wa ku Anatoti,+ m’dziko la Benjamini,+ pakuti iweyo ndi amene uli ndi ufulu woulandira monga cholowa ndiponso uli ndi ufulu wougula. Uugule ndithu.” Atatero ndinadziwa kuti mawu amenewa anali a Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena