Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Ezara 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako iwo anachita chikondwerero cha misasa+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa.+ Pachikondwererochi, anthuwo anali kubweretsa nsembe zopsereza paguwa lansembe tsiku ndi tsiku, mogwirizana ndi lamulo la nsembe zimene zinayenera kuperekedwa tsiku lililonse.+
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
4 Kenako iwo anachita chikondwerero cha misasa+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa.+ Pachikondwererochi, anthuwo anali kubweretsa nsembe zopsereza paguwa lansembe tsiku ndi tsiku, mogwirizana ndi lamulo la nsembe zimene zinayenera kuperekedwa tsiku lililonse.+