Numeri 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Komabe, ngati mkazi walonjeza ali m’nyumba ya mwamuna wake, kapena ngati wachita lonjezo lodzimana+ mwa kulumbirira moyo wake, Numeri 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwamuna wake ali ndi mphamvu zokhazikitsa kapena kufafaniza lonjezo lililonse la mkazi wake, kapenanso lumbiro la mkaziyo lodzimana, losautsa moyo wake.+
10 “Komabe, ngati mkazi walonjeza ali m’nyumba ya mwamuna wake, kapena ngati wachita lonjezo lodzimana+ mwa kulumbirira moyo wake,
13 Mwamuna wake ali ndi mphamvu zokhazikitsa kapena kufafaniza lonjezo lililonse la mkazi wake, kapenanso lumbiro la mkaziyo lodzimana, losautsa moyo wake.+