Numeri 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Iwe udzakhala wopanda cholowa m’dziko mwawo, ndipo sudzapatsidwa gawo lililonse pakati pawo.+ Ine ndine gawo lako ndi cholowa chako pakati pa ana a Isiraeli.+ Numeri 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamphatso zonse zosiyanasiyana zoperekedwa kwa inu, inunso muziperekapo chopereka kwa Yehova. Muzipereka gawo lake labwino koposa,+ monga chinthu chopatulika chimene iwo apereka.’
20 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Iwe udzakhala wopanda cholowa m’dziko mwawo, ndipo sudzapatsidwa gawo lililonse pakati pawo.+ Ine ndine gawo lako ndi cholowa chako pakati pa ana a Isiraeli.+
29 Pamphatso zonse zosiyanasiyana zoperekedwa kwa inu, inunso muziperekapo chopereka kwa Yehova. Muzipereka gawo lake labwino koposa,+ monga chinthu chopatulika chimene iwo apereka.’