Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho asalandire cholowa pakati pa abale awo. Yehova ndiye cholowa chawo,+ monga mmene anawauzira.

  • Yoswa 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Fuko la Alevi lokha ndi limene sanalipatse cholowa cha malo.+ Cholowa chawo ndicho nsembe zotentha ndi moto+ zoperekedwa kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli, monga mmene anawalonjezera.+

  • Yoswa 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Alevi alibe gawo pakati panu,+ chifukwa cholowa chawo ndi unsembe wa Yehova.+ Fuko la Gadi, Rubeni,+ ndi hafu ya fuko la Manase+ analandira kale cholowa chawo, chimene Mose mtumiki wa Yehova anawapatsa kutsidya la kum’mawa la Yorodano.”+

  • Ezekieli 44:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “‘Ponena za cholowa chawo, ineyo ndiye cholowa chawo.+ Anthu inu musawapatse chilichonse kuti chikhale chuma chawo mu Isiraeli, chuma chawo ndine.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena