Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+ Deuteronomo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Nyamukani, muyende ndi kudutsa chigwa cha Arinoni.+ Taonani, ndapereka m’manja mwanu Sihoni,+ Mwamori, mfumu ya Hesiboni. Yambani kulanda dziko lake, ndipo menyanani naye nkhondo. Deuteronomo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
24 “‘Nyamukani, muyende ndi kudutsa chigwa cha Arinoni.+ Taonani, ndapereka m’manja mwanu Sihoni,+ Mwamori, mfumu ya Hesiboni. Yambani kulanda dziko lake, ndipo menyanani naye nkhondo.
18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+