Genesis 46:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+ Deuteronomo 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ziweto zokha n’zimene tinatenga monga zofunkha pamodzi ndi zofunkha za m’mizinda imene tinalanda.+
34 Inu mukayankhe kuti: ‘Akapolo anufe takhala tikuweta ziweto kuyambira tili ana kufikira lero, ifeyo ndi makolo athu omwe.’+ Mukayankhe choncho kuti mukhale ku Goseni,+ chifukwa aliyense woweta nkhosa Aiguputo amanyansidwa naye.”+
35 Ziweto zokha n’zimene tinatenga monga zofunkha pamodzi ndi zofunkha za m’mizinda imene tinalanda.+