Numeri 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anapitiriza kunena kuti: “Ngati mungatikomere mtima atumiki anufe, mutipatse dzikolo ngati cholowa chathu. Tisawoloke nawo Yorodano.”+
5 Anapitiriza kunena kuti: “Ngati mungatikomere mtima atumiki anufe, mutipatse dzikolo ngati cholowa chathu. Tisawoloke nawo Yorodano.”+