Numeri 33:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, n’kukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu. Deuteronomo 32:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo ukafera m’phiri limene ukukwera ndi kugona ndi makolo ako,+ monga mmene Aroni m’bale wako anafera m’phiri la Hora+ ndi kugona ndi makolo ake.
37 Pambuyo pake ananyamuka ku Kadesi, n’kukamanga msasa kuphiri la Hora,+ kumalire ndi dziko la Edomu.
50 Pamenepo ukafera m’phiri limene ukukwera ndi kugona ndi makolo ako,+ monga mmene Aroni m’bale wako anafera m’phiri la Hora+ ndi kugona ndi makolo ake.