Numeri 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anapitiriza kunena kuti: “Ngati mungatikomere mtima atumiki anufe, mutipatse dzikolo ngati cholowa chathu. Tisawoloke nawo Yorodano.”+ Numeri 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tidzawoloka ndi zida kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova kudziko la Kanani.+ Ndipo tidzalandira cholowa chathu tsidya lino la Yorodano.”+
5 Anapitiriza kunena kuti: “Ngati mungatikomere mtima atumiki anufe, mutipatse dzikolo ngati cholowa chathu. Tisawoloke nawo Yorodano.”+
32 Tidzawoloka ndi zida kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova kudziko la Kanani.+ Ndipo tidzalandira cholowa chathu tsidya lino la Yorodano.”+