Numeri 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi.+ Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi. Yoswa 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Fuko la Manase, mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase,+ bambo wake wa Giliyadi,+ anali mwamuna wamphamvu pankhondo,+ ndipo gawo lake linali Giliyadi+ ndi Basana.
29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi.+ Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi.
17 Fuko la Manase, mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase,+ bambo wake wa Giliyadi,+ anali mwamuna wamphamvu pankhondo,+ ndipo gawo lake linali Giliyadi+ ndi Basana.