Ekisodo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ukamachita kalembera pa ana a Isiraeli, + aliyense wa iwo azipereka dipo la moyo wake kwa Yehova pa nthawi yowawerengayo,+ kuti mliri usawagwere pochita kalemberayo.+
12 “Ukamachita kalembera pa ana a Isiraeli, + aliyense wa iwo azipereka dipo la moyo wake kwa Yehova pa nthawi yowawerengayo,+ kuti mliri usawagwere pochita kalemberayo.+