Numeri 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madzi a tembererowa alowe m’matumbo mwako kuti akatupitse mimba yako ndi kufotetsa ntchafu yako.” Ndipo mkaziyo aziyankha kuti: “Zikhale momwemo! Zikhale momwemo!”* Numeri 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Azimwetsa mkaziyo madzi owawa a tembererowo,+ ndipo madziwo akalowa m’thupi mwake, mkaziyo azimva ululu.
22 Madzi a tembererowa alowe m’matumbo mwako kuti akatupitse mimba yako ndi kufotetsa ntchafu yako.” Ndipo mkaziyo aziyankha kuti: “Zikhale momwemo! Zikhale momwemo!”*
24 Azimwetsa mkaziyo madzi owawa a tembererowo,+ ndipo madziwo akalowa m’thupi mwake, mkaziyo azimva ululu.