Levitiko 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako wansembe azitengako pang’ono nsembe yambewu kuti ikhale chikumbutso,+ ndipo azitentha zimene watengazo paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+ Levitiko 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akatero azibweretsa ufawo kwa wansembe, ndipo wansembeyo autape kudzaza dzanja limodzi kuti ukhale chikumbutso+ cha nsembeyo. Kenako autenthe paguwa lansembe pamene pali nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.+
9 Kenako wansembe azitengako pang’ono nsembe yambewu kuti ikhale chikumbutso,+ ndipo azitentha zimene watengazo paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yotentha ndi moto, yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+
12 Akatero azibweretsa ufawo kwa wansembe, ndipo wansembeyo autape kudzaza dzanja limodzi kuti ukhale chikumbutso+ cha nsembeyo. Kenako autenthe paguwa lansembe pamene pali nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.+