Numeri 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mkazi wa munthu angazembere mwamuna wake n’kumuchimwira+ Numeri 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wansembeyo azilumbiritsa mkaziyo, pomuuza kuti: “Ngati mwamuna aliyense sanagone nawe, ndipo ngati sunam’zembere mwamuna wako pamene uli m’manja mwake,+ n’kuchita chodetsa chilichonse, madzi owawa obweretsa tembererowa asakuvulaze.
12 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mkazi wa munthu angazembere mwamuna wake n’kumuchimwira+
19 “‘Wansembeyo azilumbiritsa mkaziyo, pomuuza kuti: “Ngati mwamuna aliyense sanagone nawe, ndipo ngati sunam’zembere mwamuna wako pamene uli m’manja mwake,+ n’kuchita chodetsa chilichonse, madzi owawa obweretsa tembererowa asakuvulaze.