Levitiko 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Koma ngati akubweretsa nkhosa+ monga nsembe yake yamachimo, azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi yopanda chilema.+ Levitiko 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno azibweretsa kwa Yehova nsembe yake ya kupalamula+ chifukwa cha tchimo limene wachita. Azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi+ kapena mbuzi yaing’ono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.+
32 “‘Koma ngati akubweretsa nkhosa+ monga nsembe yake yamachimo, azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi yopanda chilema.+
6 Ndiyeno azibweretsa kwa Yehova nsembe yake ya kupalamula+ chifukwa cha tchimo limene wachita. Azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi+ kapena mbuzi yaing’ono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.+