Genesis 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Mulungu wandipatsa mphoto chifukwa ndapereka kapolo wanga kwa mwamuna wanga.” Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Isakara.*+ Genesis 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Isakara+ anali Tola,+ Puva,+ Yabi ndi Simironi.+ Numeri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Isakara.+ Mtsogoleri wa ana a Isakara ndi Netaneli,+ mwana wa Zuwara. Numeri 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna a Isakara+ ndi mabanja awo anali awa: Tola+ amene anali kholo la banja la Atola, Puva amene anali kholo la banja la Apuna,
18 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Mulungu wandipatsa mphoto chifukwa ndapereka kapolo wanga kwa mwamuna wanga.” Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Isakara.*+
5 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Isakara.+ Mtsogoleri wa ana a Isakara ndi Netaneli,+ mwana wa Zuwara.
23 Ana aamuna a Isakara+ ndi mabanja awo anali awa: Tola+ amene anali kholo la banja la Atola, Puva amene anali kholo la banja la Apuna,