Numeri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano atsogoleriwo anafika ndi zopereka zawo pamwambo wotsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku lodzoza guwalo. Anabweretsa zopereka zawozo kuguwa lansembe. Ezara 2:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Atsogoleri ena+ a nyumba za makolo awo+ atafika kunyumba ya Yehova+ imene inali ku Yerusalemu,+ anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwe pamalo ake.+
10 Tsopano atsogoleriwo anafika ndi zopereka zawo pamwambo wotsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku lodzoza guwalo. Anabweretsa zopereka zawozo kuguwa lansembe.
68 Atsogoleri ena+ a nyumba za makolo awo+ atafika kunyumba ya Yehova+ imene inali ku Yerusalemu,+ anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwe pamalo ake.+