Ekisodo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo Mose akangolowa m’chihema, mtambo woima njo ngati chipilala+ unali kutsika ndi kuima pakhomo la chihemacho. Zikatero Mulungu anali kulankhula+ ndi Mose. Numeri 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine nditsikira kumeneko+ kudzalankhula nawe.+ Ndidzatengako gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe n’kuuika pa iwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyang’anira anthuwo, kuti usausenze wekhawekha.+ Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+
9 Ndipo Mose akangolowa m’chihema, mtambo woima njo ngati chipilala+ unali kutsika ndi kuima pakhomo la chihemacho. Zikatero Mulungu anali kulankhula+ ndi Mose.
17 Ine nditsikira kumeneko+ kudzalankhula nawe.+ Ndidzatengako gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe n’kuuika pa iwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyang’anira anthuwo, kuti usausenze wekhawekha.+
8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+