Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Ndiyeno ubweretse Aroni ndi ana ake pakhomo+ la chihema chokumanako, ndipo uwalamule kuti asambe ndi madzi.+

  • Salimo 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndidzasamba m’manja mwanga kusonyeza kuti ndine wopanda cholakwa,+

      Ndipo ndidzayenda mozungulira guwa lanu lansembe, inu Yehova,+

  • Yesaya 52:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tembenukani! Tembenukani! Tulukani mmenemo!+ Musakhudze chinthu chilichonse chodetsedwa.+ Chokani pakati pake!+ Khalani oyera, inu amene mukunyamula ziwiya za Yehova.+

  • 2 Akorinto 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena