15 Muzidya mkate wopanda chofufumitsa masiku 7. Tsiku loyamba muzichotsa m’nyumba zanu mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa chifukwa aliyense wakudya mkate wokhala ndi chofufumitsa, kuchokera pa tsiku loyamba kukafika pa tsiku la 7,+ munthu wotero adzaphedwa kuti asakhalenso mu Isiraeli.+