Ekisodo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+ Ekisodo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho m’mwezi woyamba wa chaka chachiwiri, pa tsiku loyamba la mweziwo, anautsa chihema chopatulika.+
2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+
17 Choncho m’mwezi woyamba wa chaka chachiwiri, pa tsiku loyamba la mweziwo, anautsa chihema chopatulika.+