Ekisodo 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno pa nthawi ya ulonda wam’mawa,* Yehova ali mumtambo ndi moto woima njo ngati chipilala,+ anayang’ana gulu la Aiguputo, ndipo anachititsa Aiguputowo kusokonezeka.+ Ekisodo 40:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho. Nehemiya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo.
24 Ndiyeno pa nthawi ya ulonda wam’mawa,* Yehova ali mumtambo ndi moto woima njo ngati chipilala,+ anayang’ana gulu la Aiguputo, ndipo anachititsa Aiguputowo kusokonezeka.+
34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho.
12 Usana munali kuwatsogolera ndi mtambo woima njo ngati chipilala,+ ndipo usiku munali kuwatsogolera ndi moto woima njo ngati chipilala+ kuti uziwaunikira+ njira imene anayenera kuyendamo.