Salimo 81:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku lokhala mwezi, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+Pa tsiku looneka mwezi wathunthu, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, loimba pa tsiku la chikondwerero.+ Yoweli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+
3 Pa tsiku lokhala mwezi, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+Pa tsiku looneka mwezi wathunthu, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, loimba pa tsiku la chikondwerero.+
14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+