Genesis 43:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yosefe atakweza maso ake n’kuona mng’ono wake Benjamini, m’bale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndiye mng’ono wanu amene munali kunena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima+ mwana wanga.” Genesis 46:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Benjamini anali Bela,+ Bekeri,+ Asibeli, Gera,+ Namani,+ Ehi, Rosi, Mupimu,+ Hupimu+ ndi Aridi. Numeri 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo anali awa: Bela+ amene anali kholo la banja la Abela, Asibeli+ amene anali kholo la banja la Aasibeli, Ahiramu amene anali kholo la banja la Aahiramu,
29 Yosefe atakweza maso ake n’kuona mng’ono wake Benjamini, m’bale wake wa mimba imodzi,+ anati: “Kodi uyu ndiye mng’ono wanu amene munali kunena uja?”+ Ananenanso kuti: “Mulungu akukomere mtima+ mwana wanga.”
21 Ana a Benjamini anali Bela,+ Bekeri,+ Asibeli, Gera,+ Namani,+ Ehi, Rosi, Mupimu,+ Hupimu+ ndi Aridi.
38 Ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo anali awa: Bela+ amene anali kholo la banja la Abela, Asibeli+ amene anali kholo la banja la Aasibeli, Ahiramu amene anali kholo la banja la Aahiramu,