Numeri 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akaliza malipenga onse awiriwo, khamu lonse lizisunga pangano la msonkhano ndi iwe, ndipo lizifika pakhomo la chihema chokumanako.+ Yoweli 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa mu Ziyoni amuna inu.+ Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+
3 Akaliza malipenga onse awiriwo, khamu lonse lizisunga pangano la msonkhano ndi iwe, ndipo lizifika pakhomo la chihema chokumanako.+
15 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa mu Ziyoni amuna inu.+ Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+