Numeri 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atatero, anasonkhanitsa anthu onse pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri. Anawasonkhanitsa n’cholinga chakuti awalembe m’kaundula+ kuti adziwe mibadwo yawo malinga ndi mabanja awo, ndiponso nyumba za makolo awo. Anawalemba mayina kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ mmodzi ndi mmodzi. Deuteronomo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Nonsenu mwaima pano lero pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu atsogoleri a mafuko, akulu anu, atsogoleri anu, mwamuna aliyense wa mu Isiraeli,+ Yeremiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
18 Atatero, anasonkhanitsa anthu onse pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri. Anawasonkhanitsa n’cholinga chakuti awalembe m’kaundula+ kuti adziwe mibadwo yawo malinga ndi mabanja awo, ndiponso nyumba za makolo awo. Anawalemba mayina kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ mmodzi ndi mmodzi.
10 “Nonsenu mwaima pano lero pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu atsogoleri a mafuko, akulu anu, atsogoleri anu, mwamuna aliyense wa mu Isiraeli,+
5 Nenani zimenezi mu Yuda anthu inu, ndipo zilengezeni ngakhale mu Yerusalemu.+ Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa m’dziko lonse.+ Fuulani kuti: “Sonkhanani pamodzi, ndipo tiyeni tilowe m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+