Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zitatero, Rakele anati: “Mulungu wakhala monga woweruza+ wanga ndipo wamvera mawu anga, choncho wandipatsa mwana wamwamuna.” N’chifukwa chake Rakele anatcha mwanayo dzina lakuti Dani.*+

  • Genesis 46:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ana a Dani+ anali Husimu.*+

  • Numeri 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Chigawo cha mafuko atatu cha Dani ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kumpoto. Mtsogoleri wa ana a Dani ndi Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.

  • Numeri 10:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pomaliza, a m’chigawo cha mafuko atatu cha ana a Dani+ ananyamuka. Iwo ndiwo anali olonda kumbuyo kwa zigawo zonse za mafukowo.+ Mtsogoleri wa asilikali awo anali Ahiyezeri,+ mwana wa Amisadai.

  • Numeri 26:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Ana aamuna a Dani+ mwa mabanja awo anali ochokera kwa Suhamu amene anali kholo la banja la Asuhamu. Awa anali mabanja a Dani+ potsata fuko lawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena