Ekisodo 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri. Levitiko 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno panali mnyamata wina amene mayi wake anali Mwisiraeli, koma bambo wake anali Mwiguputo.+ Mnyamatayu analowa pakati pa ana a Isiraeli ndipo anayamba kulimbana ndi Mwisiraeli+ wina mumsasa.
38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri.
10 Ndiyeno panali mnyamata wina amene mayi wake anali Mwisiraeli, koma bambo wake anali Mwiguputo.+ Mnyamatayu analowa pakati pa ana a Isiraeli ndipo anayamba kulimbana ndi Mwisiraeli+ wina mumsasa.