Levitiko 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno panali mnyamata wina amene mayi ake anali a Chiisiraeli, koma bambo ake anali a ku Iguputo.+ Mnyamatayu anayamba kumenyana ndi munthu wina wa Chiisiraeli mumsasa.
10 Ndiyeno panali mnyamata wina amene mayi ake anali a Chiisiraeli, koma bambo ake anali a ku Iguputo.+ Mnyamatayu anayamba kumenyana ndi munthu wina wa Chiisiraeli mumsasa.