Salimo 78:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anapitiriza kuyesa Mulungu m’mitima yawo+Mwa kupempha chakudya china chimene mtima wawo unalakalaka.+ Salimo 78:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti iwo sanakhulupirire Mulungu.+Sanakhulupirire kuti iye adzawapulumutsa.+ Salimo 106:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anasonyeza chikhumbo chawo chadyera m’chipululu,+Ndipo anayesa Mulungu m’chipululumo.+
18 Iwo anapitiriza kuyesa Mulungu m’mitima yawo+Mwa kupempha chakudya china chimene mtima wawo unalakalaka.+